Lyrics

Panado panado yeah mmm ma headache yeah mmm eeh Panado panado mmm eeh Amakonda miseche Amakondwa munthu adzivutika Zochitika ngati siopemphera Daily daily busy ntopola Kubaya ma damage Kuupasa moyo wanga challenge Machitidwe awo ngati Judas Makhalidwe awo ngati njenjete eeh Amafuna ndikokoloke Amakhumbira nditaphokoloka Amafuna ndisokoloke Amafuna mwina nditakomoka Amafuna ndikokoloke Amakhumbira nditaphokoloka Amafuna ndisokoloke Amafuna mwina nditakomoka Ndi nsanje apatseni, panado panado Panado panado Amweko panado panado Panado anado Mutu wakula ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka mwina ndi nsanje Kaduka, mtima wachigawega Mutu wakula ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka, mtima wachigawega Samafuna ndiyendere njale Samakondwa ndikamadya money Zikandiyendera amakoka chibale Zikamandivuta andinyoza kumbali Koma mulungu andichita balance, I relax Amamenya nkhondo nditakhala pansi Adani anga onse alemba m'madzi Samakondwa nane Amafuna ndikokoloke Amakhumbira nditaphokoloka Amafuna ndisokoloke Amafuna mwina nditakomoka Amafuna ndikokoloke Amakhumbira nditaphokoloka Amafuna ndisokoloke Amafuna mwina nditakomoka Ndi nsanje apatseni, panado panado Panado panado Amweko panado panado Panado panado Mutu wakula ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka mwina ndi nsanje Kaduka, mtima wachigawega Mutu wakula ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka, mtima wachigawega
Writer(s): Armstrong Kalua Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out