音乐视频
Sir Paul Banda 的热门歌曲
制作
出演艺人
Sir Paul Banda
表演者
作曲和作词
Sir Paul Banda
作曲
制作和工程
Sir Paul Banda
制作人
歌词
Kale munali ana aulemu
Lero dziko latembenuka inde
Mulimbana ndi makolo anu
M'malo mowapatsa ulemu inde
Mwaphunzira kumwa mowa ndi kusuta
Aphunzitsi simuwona ngati kanthu inu
Mwataya mwambo wamakolo athu
Ndi makhalidwe anu amakono inu
Tinali kulemekeza makolo
Tinali omvera pa zonse ife
Tinali okondana ndi amzathu
Olimbikira pa za Mulungu ife
Akulu mphavu zawo zikutha
Aphunzitsi adotolo a m'mawa ndinu
Inu atsogoleri a m'mwawa
Konzani tsogolo lokoma inu
Dzidzimuka mnyamata iwe
Galamuka iwe nsungwana chonde
Kumbukira chikhalidwe cha makolo
Ndinu atsogoleri a m'mawa inu
Konzani moyo
Inu achinyamata
Tinyadire
Dziko lathu
Tigwire ntchito
Kukonza tsogolo
Dziko la m'mawa
Lidzakhale lokoma
Konzani moyo
Inu achinyamata
Tinyadire
Dziko lathu
Tigwire ntchito
Kukonza tsogolo
Dziko la m'mawa
Lidzakhale lokoma
Konzani moyo
Inu achinyamata
Tinyadire
Dziko lathu
Tigwire ntchito
Kukonza tsogolo
Dziko la m'mawa
Lidzakhale lokoma
Konzani moyo
Inu achinyamata
Tinyadire
Dziko lathu
Tigwire ntchito
Kukonza tsogolo
Dziko la m'mawa
Lidzakhale lokoma
Writer(s): Sir Paul Banda
Lyrics powered by www.musixmatch.com