制作
出演艺人
Marco Sadik
表演者
作曲和作词
Marco Sadik
词曲作者
歌词
Ngati chikondi m'mati chokoma
Nanga ine bwanji kuwawa oh
Bwenzi langa linali lokonda
Mwalinamiza lelo lapita
Kani ntimawanu ngoyipa inu
Mulingati njoka mu udzu
Ndazindikila yemwe amakupha
Ndiodya naye mbale imodzi
Chilichonse ndingapange mungonyoza
Kulikonse mungapite mungolonda
Anthu antundu wanji inu abodza
Mutileke mutisiye
Takondana basi
Takondana basi
Linda bwelela tizamange banja
Chonde pilila tizasungane
Chikondi ndi anthu awili enawa mabodza
Wachitatu bwenzi langa osokoneza
Amamasula amakaniza usamumvele
Ngati uli undeta wakukwana
Iwe tangoleka nsanje yako
Ungotaya nthawi yako pa chabe
Yesetsa kufuna uzapeza
Ngati ukumakala kusowa chochita
Paliponse ungayende ungobwebweta
Chita manyazi ndipatse danga
Uyu ndi wanga okondendwa
Chilichonse ndingapange mungonyoza
Kulikonse mungapite mungolonda
Anthu antundu wanji inu abodza
Mutileke mutisiye
Takondana basi (oh no)
Takondana basi
Linda bwelela tizamange banja
Chonde pilila tizasungane
Chikondi ndi anthu awili enawa mabodza
Wachitatu bwenzi langa ndiosokoneza
Amamasula amakaniza usamumvele
Pamene bwenzi lapita inu chimwemwe kusaya
Kusangala kuti ine pamudzi ndikhale ndekha
Komabe ndimuyitana iye abwelela
Linda (iwe Linda bwelela iwe)
Linda (iwe Linda bwelela iwe)
Linda (iwe Linda bwelela iwe)
Linda (chonde nkazi wanga)
Linda bwelela tizamange banja
Chonde pilila tizasungane
Chikondi ndi anthu awili enawa mabodza
Wachitatu bwenzi langa ndiosokoneza
Amamasula amakaniza usamumvele
Ndatopa nawo mabodza
Dona yanga iyo
Isiyeni yokha
Nanenso
Ndisiyeni ndekha
Linda (iwe Linda bwelela iwe)
Linda (iwe Linda bwelela iwe)
Chikondi ndi anthu awili
Chikondi ndi anthu awili
Chikondi ndi anthu awili
Written by: Marco Sadik