制作

作曲和作词
Kelvin Zalimba
Kelvin Zalimba
词曲作者
dumisani Moyo
dumisani Moyo
词曲作者
制作和工程
Blage
Blage
制作人
M.anifest
M.anifest
母带工程师

歌词

Lero ndi tsiku lomwe Yehovah wapanga
Inu Tikondwelele
Tiyeni tisekelele
Lero ndi tsiku lomwe Yehovah wapanga
Tiyeni tikondwelele (Chimwemwe)
Tiyeni tisekelele (Chimwemwe)
Wayiwala kale langa
Wayitana Dzina langa
Ine Ndavomela
Ine Ndavomela ahh
Wayiwala kale langa
Wayitana Dzina langa
Ine Ndavomela
Ndeno kumwambako
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Kumwamba Chimwemwe (chimwemwe chimwemwe)
Mtima wanga Chimwemwe (chimwemwe chimwemwe)
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Yesu wanga ondisamala
Mwazi wake wandiyeretsa
Chisomo chake chandiitana
Mtima wanga Chimwemwe
Ntchito zanga zomwe amakonda
Anaika mu folder
Nandiyang'ana mokondwa
Everything in order
Wayiwala kale langa
Wayitana Dzina langa
Ine Ndavomela
Ine Ndavomela ahh
Wayiwala kale langa
Wayitana Dzina langa
Ine Ndavomela
Ndeno kumwambako
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Kumwamba Chimwemwe (chimwemwe chimwemwe)
Mtima wanga Chimwemwe (chimwemwe chimwemwe)
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
Chimwemwe Chimwemwe Chimwemwe
There's a party in heaven
Everytime a sinner's saved
Yeah the Lord has called my name
Mtima wanga celebrate (celebrate)
There's a party in heaven
Everytime a sinner's saved
Yeah the Lord has called my name
Mtima wanga celebrate
Written by: Kelvin Zalimba, dumisani Moyo
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...