制作
出演艺人
Teddy Makadi
声乐
Dan Khoviwa
键盘
Judah Mkandawire
贝斯
AB Malinga
原声吉他
作曲和作词
Teddy Maliza
词曲作者
制作和工程
Dan Khoviwa
工程师
ViddiX
制作人
Melma
制作人
歌词
Please don't cry
Please don't cry no
Anakuswela wako mtima koma
Dziwa uzayiwala izo
Baby usalire
Pukuta misonzi
Sindikondwa ukalira
Ndimafuna uziseka nawo
So I don't wanna see you crying
Oh crying for love
Zimachitika mmomwe umazinvera
Nane ena mtima mpaka anasiya chilema
But baby, just don't cry no
Crying for love
Ukazapola wako mtima
Uzadziwa it's a waste of time
You you you
You deserve a loving
Yoti ukakamba za ku mtima
Munthu wako azikumvera
Baby such a loving
Yoti ukamupatsa nthawi
Naye azitha kubwenzera
A special kind of loving
Simachita kufuna special planning no way
Zonse zimatheka ndi nthawi
Nawenso yako izafika
So I don't wanna see you crying
Oh crying for love
Zimachitika mmomwe umazinvera
Nane ena mtima mpaka anasiya chilema
But baby, just don't cry no
Crying for love
Ukazapola wako mtima
Uzadziwa it's a waste of time
Dziwa it's a waste of time oh oh oh
Dziwa it's a waste of time uh uh uh
Written by: Teddy Maliza