album cover
Mtima
321
Afro-Beat
Mtima 由 Deebo Creatives 于 2025年6月12日 发行,作为专辑“First Born”的一部分。
album cover
发行日期2025年6月12日
唱片公司Deebo Creatives
旋律性
不插电
Valence
舞蹈性
能量
BPM93

歌词

Its, Emmie, again (It's Macia, the rhythm boy)
Deebo!
Butterflies all over in my belly
Ndikamuna goosebumps on my body
Koma ndimazakumbukila kuti natengedwa kale
Wanga ndinampeza kale
Mtima wangokhala osakhutitsidwa
Zimandiwawa kulimbana nawo mtimawu
Kuyesa kudziletsa
Koma nkhope yake imangobwelabe
Ndimangolotabe kumango ganizabe za iye
Mwina ndinachita phuma kodi?
Nthiti yanga nayisempha kodi?
Nditengele za mtima kodi?
I don't know what to do
Mtima wanga bwanji umandizumza chonchi iwe?
Mtima wanga bwanji sumakhuta nchimodzi iwe?
Uzandipalamulitsa iwe
Uzandiika mmavuto iwe
Uzandipalamulitsa iwe
Uzandiyika m'mavuto
Mtima wanga dekha
Poyamba ndinkafuna Peshe
Kenako ndinkafuna Benja
Lelo ndamupeza komabe mtima sukhutila
Ndikaona Mphatso mtima umachita tunthumila
Aaah Aaah! Eee!
Zofuna mtima zimabwelabe
Ukazipeza umasakabe
Zofuna mtima zimabwelabe
Ukazipeza sizikwana
Aaaaa! Aaaah!
Mtima uzandiphetsa, uzandiphetsa!
Aaaa! Aaaah! Ndizapalamula, palamula
Mtima wanga bwanji umandizumza chonchi iwe?
Mtima wanga bwanji sumakhuta nchimodzi iwe?
Uzandipalamulitsa iwe
Uzandiika mmavuto iwe
Uzandipalamulitsa iwe
Uzandiyika m'mavuto
Mtima wanga dekha
Mtima wanga bwanji umandizumza chonchi iwe? (Mtima wangaaa)
Mtima wanga bwanji sumakhuta nchimodzi iwe? (Oooh uuhooh)
Uzandipalamulitsa iwe
Uzandiika mmavuto iwe
Uzandipalamulitsa iwe
Uzandiyika m'mavuto
Mtima wanga dekha
Written by: Emily Zintambira
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...