積分
詞曲
Shafie Phiri
詞曲創作
製作與工程團隊
Fat Nyanda
製作人
Taktic
共同製作人
歌詞
Akakhala mantha
Ndiye bwenzi langa
Usiku umatalika
Ndiye ndimapaopa panja
Anzanga ndi ambiri
Koma ndi odziwana nawo ah oh
Mama lift us years ago
Pano timaziona tokha
I'm losing hope, I'm losing faith, I'm losing myself
I'm breeding out, my wounds are open
But i can't surrender
I'm losing hope, I'm losing faith, I'm losing myself
I'm breeding out, my wounds are open
But God will make a way
Nkona tipemphera
Ambuye mutimvera
Kwa Inu mkothawira
Mutipatse njira ooh
God will make a way
God will make a (mmmh)
God will make a way
God will make a (mmmh)
God will make a way
God will make a (mmmh)
God will make a way
God will make a (mmmh)
I'm a boy from a village
I just wanna get a dream
Don't get in my way
Staying a couple of days opanda chakudya
Ndikugonera madzi
Tikagwa timadzikoka
Umakhala mwayi osakomoka
Poti mavuto amatiopsa amama
Tikagwa timadzikoka
Umakhala mwayi osadzipha
Poti mavuto omwe timaona
I'm losing hope
I am losing faith
Ambuye mukundimva kodi?
Ine mwana wanu pano, Ambuye
Nkona tipemphera
Ambuye mutimvera (aah mutimvere)
Kwa Inu mkothawira
Mutipatse njira ooh
God will make a way (God will make a way)
God will make a (mmmh)
God will make a way (God will make a way)
God will make a (mmmh)
God will make a way (God will make a way)
God will make a (mmmh)
God will make a way (God will make a way)
God will make a (mmmh)
Yeah, yeah yeah, yeah!
Oooh (God will make a way)
Written by: Shafie Phiri