音樂影片

音樂影片

積分

演出藝人
Madalitso Band
Madalitso Band
演出者
Yobu Maligwa
Yobu Maligwa
聖歌聲樂
Yosefe Kalekeni
Yosefe Kalekeni
聖歌聲樂
詞曲
Yobu Maligwa
Yobu Maligwa
作曲
Yosefe Kalekeni
Yosefe Kalekeni
作曲
製作與工程團隊
Madalitso Band
Madalitso Band
製作人
Benoit Bel
Benoit Bel
母帶工程師
Johannes Buff
Johannes Buff
混音師

歌詞

Ine, ako
Ine, ako
Ine, ako
Ine, ako
Ine, ayayay
Ine, ako
Anafera chiyani kodi? Anfera chiboda
Anafera chiyani mayi? Anfera chiboda
Anafera chiyani kodi? Anfera chiboda
Anafera chiyani khaze? Anafera chiboda
Ena si awo? Anafera chiboda
Ena si awo? Anafera chiboda
Taona, anafera chiboda
Taona, anafera chiboda
Anfera chiyani kodi? Anafera chiboda
Panali mtsikana wina
Panali mtsikana wina
Amene ankafuna banja
Amene ankafuna banja
Ati mamuna amukwatire
Ati mamuna amukwatire
Koma kamunayo akhale wachuma
Koma kamunayo akhale wachuma
Kumakana amuna osauka
Kumakana amuna osauka
Wayiwala banja si chuma
Banja ku khumudwitsana
Ine, ako
Ine
Anafera chiyani kodi? Anfera chiboda
Anafera chiyani mayi? Anfera chiboda
Anafera chiyani kodi? Anfera chiboda
Anafera chiyani khaze? Anafera chiboda
Ena si awo? Anafera chiboda
Ena si awo? Anafera chiboda
Taona, anafera chiboda
Taona, anafera chiboda
Anfera chiyani kodi? Anafera chiboda
Anafera chiyani kodi? Anfera chiboda
Anafera chiyani mayi? Anfera chiboda
Anafera chiyani kodi? Anfera chiboda
Anafera chiyani khaze? Anafera chiboda
Ena si awo? Anafera chiboda
Ena si awo? Anafera chiboda
Taona, anafera chiboda
Anfera chiyani kodi? Anafera chiboda
Written by: Yobu Maligwa, Yosefe Kalekeni
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...