歌詞
Nalelo kwacha lelo nayenda kuti nichita chani
Imweh kwacha lelo siniziba ezankala bwanji
Imwe kwacha lelo oooooo kulibe poyambila emweee
Niziba imavuta, niziba imakosa imavuta nokukontola
Kuyesa ni mayesa, kuyesa ni mayesa imavuta che kukontolola
Muziti pempelelako, muziti pempelelako ise
Muziti pempelelako, muziti pempelelako ise
Muziti pempelelako, muziti pempelelako ise
Muziti pempelelako, muziti pempelelako ise
Ohooooo , ohooooo ise oh yea
Oh noooo oh oh, sinifuna naku yangana,
The ones you call your friends today are never even there when you need them.
Mmmmmmmm some people are wicked when your life is on fire, when your life is on fire
Muziba nimayesa, kuyesa nimayesa imavuta che kukontola
Keep your strength and hold on tight
In the dark there's always a little light
Lift your spirit when you're feeling low
Through the storm, you will glow
Muziti pempelelako, muziti pempelelako ise
Muziti pempelelako, muziti pempelelako ise
Muziti pempelelako, muziti pempelelako ise
Muziti pempelelako, muziti pempelelako ise
Written by: Emmanuel Hakanzaba