積分

演出藝人
Lucius Banda
Lucius Banda
演出者
詞曲
Lucius Banda
Lucius Banda
作曲

歌詞

Ngati kumwambako kuli ma ukwati
Mkayesetsa kukhala oyamba kukufusira
Ukakhale mkazi wanga
Mtima wako, maonekedwe
Mayankhulidwe ngakhale poyenda
Ndiwetu angel wangotsala mapiko hey
Takula limodzi kuyambira umwana aha
Tapanga chibwenzi moyo wathu onse aha
Umkafuna banja Ine ndimkazemba aha
Anzathu achangu angoti wanga buu wo-wo-woo
Wamasuka mkazi uja
Wakwatiwa bwezi langa
Zikundiwawa kuti wandithawadi
Moyo winawo mwinatu zidzayenda
Wamasuka mkazi uja
Wakwatiwa bwezi langa
Zikundiwawa kuti wandithawadi
Moyo winawo mwinatu zidzayenda
Poti chitsime chimadziwika
Kuti ndichakuya pomwe chawuma
Mkazi wabwino umad'ziwa akapita
Moyo winanwo ndidzayesetsa
Kuchita zomwe utadzafune
Poti panopa ndiwe mkazi wamwini (hey-hey-hey-hey)
Takula limodzi kuyambira umwana aha
Tapanga chibwenzi moyo wathu onse aha
Umkafuna banja Ine ndimkazemba aha
Anzathu achangu angoti wanga buu wo-wo-woo
Wamasuka mkazi uja
Wakwatiwa bwezi langa
Zikundiwawa kuti wandithawadi
Moyo winawo mwinatu zidzayenda (mwina, mwina, mwina, mwina)
Wamasuka mkazi uja
Wakwatiwa bwezi langa
Zikundiwawa kuti wandithawadi
Moyo winawo mwinatu zidzayenda
Anyamata lero mukumaonjeza
Kufuna banja koma kunjoya
Mukamuvula mumamtaya ngazi sanza
Iwe daughter wanga bwenzi lakolo
Ngati akukonda adzadikilira
Ndiwetu duwa lero mawa wafota oow
Takula limodzi kuyambira umwana aha
Tapanga chibwenzi moyo wathu onse aha
Umkafuna banja Ine ndimkazemba aha
Anzanga achangu angotipanga buu wo-wo-woo
Wamasuka mkazi uja
Wakwatiwa bwezi langa (bwenzi langa)
Zikundiwawa kuti wandithawadi (zikundiwawa mama)
Moyo winawo mwinatu zidzayenda (ngati uli ukwati mama)
Wamasuka mkazi uja (ooh mkazi wanga)
Wakwatiwa bwezi langa (ulendo)
Zikundiwawa kuti wandithawadi (wapita)
Moyo winawo mwinatu zidzayenda (oh iyo ma-ma-ma-ma)
Written by: Lucius Banda
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...