Lyrics

Woyee yeah yeah Osamayiwala kwanu Osamayiwala Kwanu Ndi Kwanu mhuu Nthengo mudalaka njoka aaah Kwanu Ndi Kwanu mhuuu Nthengo mudalaka njoka aaah Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh Ndi kwanube Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh Ndi kwanube Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh Ndi kwanube Nthengo mudalaka njoka aaah Penapake zikavuta iwe Ndikwanube Usamachite manyazi Ndikwanube Utha kubwerera konko Ndikwanube ah ah aaaaah Osayi wala Dzuwa likawala Yemwe anakubala Yemwe anakusamala Pamene ukudwala Usanakwela ladder Kwanu kwanu nthengo mudalaka njoka Uzakufunabe olo utachoka Mukanyozela muzatenga matsoka Osalora azako aziku locker Kwanu Ndi Kwanu mmhu Nthengo mudalaka njoka aah Kwanu Ndi Kwanu mhuu Nthengo mudalaka njoka aaah Munachoka kunyumba kalekale mwati munatola Ka joker Koma muzabwerabe kwanu nthengo munalaka Ka njoka Mwasintha mawanga mwasintha khungu mapeto Ake ndi matsoka Muzatipeza zinthu zikazavuta Pano tingopenya ndi maso Pa maliro simumapezeka Kumanda simumapezeka Koma kuti mugone pansi lero lomwe kumanda omwewo mupezeka Anapita kalekale kokawonekela eh Koma kaphiri kakwawo sikaonekela eh Pena nkumati njokayo mwina nthengo yasochela Koma azatipezabe mizimu sikukondwera Kwanu Ndi Kwanu mmhu Nthengo mudalaka njoka aah Kwanu Ndi Kwanu mhuu Nthengo mudalaka njoka aaah Yeah Galu amanyada pakwawo nanga iweyo ulekelanji Uzigomela Malawi kwanu kuno sungasowe mtaji Funsa neba amasililanji Mtendere umayambila chitipa kuthela Ku nsanje Warm heart Ku mpanje Uzingotakata mpakana uzatsegula maloko Kutukula Dela lakwanu akhale ako maloto Kwanu usakuluzile hope Ukavaya abroad kusaka guap Tsiku lomwe uzafike pa top Kwanu uzakuyikeso pa map Mukanabwera Mwakhalitsa Anzanu ochenjela Goshen amangitsa Lemme explain Kulibeko Malo ngati pa den Tufunika mindset change Osangokhalila kupanga complain Yeah yeah Kwanu Ndi Kwanu mhuu Nthengo mudalaka njoka aaah Kwanu Ndi Kwanu mhuuu Nthengo mudalaka njoka aaah Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh Ndi kwanube Kwanu Ndi Kwanu mhhu eh Ndi kwanube Kwanu Ndi Kwanu mmhu eh Ndi kwanube Nthengo mudalaka njoka aaah Kamdothi iwe bwerera Ku nyumba iwe Kamdothi iwe uthela moyenda iwe Kamdothi iwe aaaaaah Kamdothi iwe aaaaaah Kwanu Ndi Kwanu mfana Town ikasolobana Ukumbuke padzana Bwerera Kwa Amama
Writer(s): Joy Gondwe Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out