Lyrics

Blood is thicker than water Family is all that matter I'll always love you harder indee Ndinu abale anga inu Ndinu abale anga inu Munadusa pokhala anzanga inu Mumaukomesa moyo wanga inu Agulu langa inu Olo tisemphane simundituluka Olo ndikunyozeni mumakhululuka Inde kusemphana sikumalephelera Mu umodzi muli mphavu abale kumandipemphelera Family is supposed to be supportive No negative vibe all love Family is a bond made on earth and above If family is like a pool then let us all dive Let us all dive Nde osamadana osajedana Kumakondana pachibale osaphana Chibale ndi chipyela sumangogwela Umodzi usathe Kholo kumawamvela Zikalakwika kumauzana chonde Tizachita bwino ngati nthaka ya chonde Ka get together bwa? Tikacheze pakhonde Kuli matenda, tiyeni tonse tikazonde Ndinu abale anga inu Ndinu abale anga inu Munadusa pokhala anzanga inu Mumaukomesa moyo wanga inu Agulu langa inu Ndikawina Nanuso! Ndikagula Njale Njanuso! Ndikamanga Den Nkwanuso! Olo ndikapeza Nkazi Mmmh mmmh Chibale chipyela Tingasemphane chilibe pothela Tingatulukane kukonda adela Ndizathamangila Iwe vuto likandigwela Mmmh you are my blood O+ If I got ill no fuss Pena ndiwe poison pena ndiwe charm Walter Nyamilandu I'm just stuck with FAM Nditha kukhala mwezi osakukhola Chibale sichimatha osachitola Kapena osachitaya Zima day ones osazitaya Blood is thicker than water Family is all that matter I'll always love you harder indee Ndinu abale anga inu Ndinu abale anga inu Munadusa pokhala anzanga inu Mumaukomesa moyo wanga inu Agulu langa inu Ndinu abale anga inu
Writer(s): Smart Banda Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out