album cover
Ntchito
album cover
Ntchito wurde am 16. Mai 2025 von Royal Image als Teil des Albums Cifu veröffentlicht
AlbumCifu
Veröffentlicht16. Mai 2025
LabelRoyal Image
BPM134
Melodizität
Akustizität
Valence
Tanzbarkeit
Energie

Songtexte

Whoa yah!
Kumati kukangoda
Aunt Mwandida amaziphodaphoda
Masana sanali ochulukidwa
Amkati ntchito yawo imayamba mochedwa (mmh)
Kumati kukangoda
Aunt Mwandida amaziphodaphoda
Atatchena nsalu kumanyamukidwa
Pakhomo pawo timasamalidwa
Ndi ntchito yawo (ooh-oh)
Ntchito yawo (ooh-oh)
Ntchito yawo (ooh-oh)
Ntchito yawo (ooh-oh)
Ku ntchito yawo
Phone imakhala busy
Aunt ntchito amagwira ndima biggy
Akayankha amati ali mu meeting
Pansi pakumveka nyimbo, Gibo Pearson
Aunt anga anali munthu olimbikila
Ali moyo sitimkagona ndi njala
Atatisiya, ambili anawalira
Koma chodabwitsa olo munthu m'modzi
Waku ntchito kwawo (ooh-oh)
Ku ntchito kwawo (ooh-oh)
Waku ntchito kwawo (ooh-oh)
Ku ntchito kwawo (ooh-oh)
Ku ntchito kwawo
Ali moyo amkatengedwa m'ma prado (awo!)
Akamabwela amkatsika muchi D4D (awo!)
Zodabwitsa tsiku la maliro awo
Sim'daonepo galimoto imodzi
Zimandikhudza heavy
Mabwana awo sadadzaonekele
Aunt Mwandida, anasiya ana
Mpaka pano pension siyidafike
Ya ntchito yawo (ooh-oh)
Ntchito yawo (ooh-oh)
Ntchito yawo (ooh-oh)
Ntchito yawo (ooh-oh)
Yeah
Mmh-mmh-mmh-mmh
Mmh-mmhu-mmh-mmh-mmmh
Mmh-mmh-mmh-mmh
Mmh-mmhu-mmh-mmh-mmh
Written by: Chifuniro Magalasi, Desire

Loading...