album cover
Soja
9.093
Afro-Beat
Soja wurde am 16. Mai 2025 von Royal Image als Teil des Albums Cifu veröffentlicht
album cover
AlbumCifu
Veröffentlichungsdatum16. Mai 2025
LabelRoyal Image
Melodizität
Akustizität
Valence
Tanzbarkeit
Energie
BPM142

Musikvideo

Musikvideo

Songtexte

Uuh-uuh, ooh!
Sa-Sa-Sa-Sa
Savage on the beat (ooh-ooh)
Naye ndi mpulumutsi
Iyeyu ndi mtetezi
Zolinga zawo nzimodzi
Amanditchinga ku mphezi
Mvura ingawombe
Kukabwera namondwe
Simchita mantha ine
Ndimadziwa pali soja ine
Left, right about turn
Ulandire ma salute
Simdziwa umakwanitsa bwanji
Mwana wanga you you support (yeah, yeah)
Left, right about turn
Ulandire ma salute
Sim'ndziwa umakwanitsa bwanji
Ndikamakhala kumudzi kuno
Sindiopa, sindiopa ayi
Sindiopa m'nyumbamu
Ndili ndi soja, ndi soja yi
Amandisunga m'nyumbamu
Sindiopa, sindiopa ayi
Sindiopa m'nyumbamu
Ndili ndi soja, ndi soja yi
Ndipo sangandisiye
Analonjeza kamodzi
Tsiku la ukwati wanga
Tidzakhala limodzi
Nkhondo yako ndi yanga
Akachoka mam'mawa
Pena ndimagwidwa chinkhawa ine
Wasiya kundisowa
Olo mwina wandithawa, iwe
(Left, right about turn) cham'ma late hour
Amuna angawa (salute)
(Left, right) amatulukira awa
Amuna angawa (ma salute)
(Left, right about turn) amamenya nkhondo zanga
Amadzetsa mtendere wanga (salute)
(Left, right) munthuyi ndi soja wanga
Olo zindivute motani
Sindiopa, sindiopa ayi
Sindiopa m'nyumbamu
Ndili ndi soja, ndi soja yi
Amandisunga m'nyumbamu
Sindiopa, sindiopa ayi
Sindiopa m'nyumbamu
Ndili ndi soja, ndi soja yi
Aaah!
Left, right about turn
Mulandire ma salute (ooh, wah)
Sim'ndziwa mumakwanitsa bwanji
Adadi anga you support (yo)
Left, right about turn (sindio-)
Mulandire ma salute (sindio-, sindio-)
Wu single parent ndimakwanitsa bwanji
Amayi anga (ay, yeah-yeah)
Kwanga ndikuthoza
Kwanga ndikuyamika
Mkona ndimapemphera
Kuti mudzimuyang'anira soja
Mudzimuyang'anira soja
Written by: Chifuniro Magalasi
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...