album cover
Kumatikhala
260
Afro-Beat
Kumatikhala wurde am 12. Juni 2025 von Deebo Creatives als Teil des Albums First Born veröffentlicht
album cover
Veröffentlichungsdatum12. Juni 2025
LabelDeebo Creatives
Melodizität
Akustizität
Valence
Tanzbarkeit
Energie
BPM113

Songtexte

Ine dzulo, ndafatsa ndekha basi
Kuziyang'anila glass
Ndadalitsidwa munthune (Aaaah)
Odalafe, ifeyo ndodalafe (odala ah)
Odalafe, ifeyo ndodala (ndiodalaaa)
Abwino, ifeyo ndabwino ehe
Abwino, ifeyo ndabwino (ndabwino)
Abwino ifeyo ndabwino ehe
Abwino ifeyo ndabwino
Kutchenako (Kumatikhala)
Kubhebhako ( kumatikhala)
Kuoneka bho (Kumatikhala)
Kuwalako Kumatikhala
Kutchenako (Kumatikhala)
Kubhebhako ( kumatikhala)
Kuoneka bho (Kumatikhala)
Kuwalako (Kumatikhala)
Ah Kumatikhala (Kumatikhala)
Kumatikhala (Kumatikhala
Kumatikhala (Kumatikhala)
Kumatikhala (Kumatikhala)
Ah Kumatikhala (Kumatikhala)
Kumatikhala (Kumatikhala)
Kumatikhala (Kumatikhala)
Kumatikhala aaa aha
Huh huhuh! Huh huhuh!
Huh huhuh! Huh huhuh!
Eyeliner, lipgloss, lipstick zimapanga magic
Ma knotless, ka ma wig onse amapanga magic
ndikati ndisambe ndiziphodeee
(Asa ona Ngenge)
Ndikati ndisambe ndizikonzeee
(Asa ona Ngenge)
Olo asanene no
Ndimadziwa ndine oneka bho
Ine ndi wabwino
With or without approval ooh
Olo asanene no
Ndimadziwa ndine oneka bho
Ine ndi wabwino
With or without approval ooh
Kutchenako (Kumatikhala)
Kubhebhako ( kumatikhala)
Kuoneka bho (Kumatikhala)
Kuwalako (Kumatikhala)
Kutchenako (Kumatikhala)
Kubhebhako ( kumatikhala)
Kuoneka bho (Kumatikhala)
Kuwalako (Kumatikhala)
Ah Kumatikhala (Kumatikhala)
Kumatikhala (Kumatikhala
Kumatikhala (Kumatikhala)
Kumatikhala (Kumatikhala)
Ah Kumatikhala (Kumatikhala)
Kumatikhala (Kumatikhala)
Kumatikhala (Kumatikhala
Kumatikhala aaa aha
Huh huhuh! Huh huhuh!
Huh huhuh! Huh huhuh!
Written by: Britain Bauleni, Emily Zintambira
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...