album cover
Z
album cover
Z è stato pubblicato il 5 aprile 2020 da 1684208 Records DK come parte dell'album The Book of Z
5 aprile 2020
Etichetta1684208 Records DK
LinguaEnglish
BPM
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia

Testi

Mic check
Mic check
One two, one two
Ase wayamba ku recorder
Aaa ok tiyeni tiyambe
Mtima ukapuma
Zichewa pakamwa
Mudzi nawo umasungulumwa
Tinali naye dzulo
Tadya naye nkhomalilo
Oh ndatopa m'masomu tulo
Tiwonana mawa ndikaone pillow
Sindikudziwa chidzanditenge ndichani
Chonde musadzalile inu
Mzimu wanga udzadzadzidwa ndichimwemwe
Musazadandaule
Awuzeni alowe
Andione nkhope komaliza
Akamaliza andipelekeze
Malo a zii wo
Awuzeni alowe andione nkophe komaliza Andipelekeze, (ine ine)
Malo a zi wo
Aay ndidzakhala pompo ndili mu form ya mzimu
Ndidzidzaona chilichonse
Osaopa sindizaona zinazo
Timiseche sindidzamva nawo
Adzukulu adzakusana makasu mammawa mwina
Azimayi masana adzayimba hosanna
Malo a zi timukonzele mudzi
Anyamata tikumbe pati
Apo ayi pali miyala
Apa bwino pali a uje
Akapume akatchole batcha ndi mbalame
Kanali ka n'yamata kokonda nthabwala
Auzeni anambe kumphikako njala, (aaa ntchito timadyela ka)
Nde ndidzidzangoseka
Malo a zi wo
Mu uzimu ndidzasuzumila kumphika
Malo a zi wo
Anambe akutsinkha ndiwo
Malo a zi wo
Ena mwa mwayi adzapeza banja
Mmm yeah malo a zi wo (malo a zi wo)
Malo a zi wo (malo a zi wo)
Malo a zi wo (malo a zi wo)
Malo a zi wo (malo a zi wo)
Ndidzamva wizulo amayi amvano
Oh kani ndimkakondedwa chonchi (malawilano)
Mayambililo tapanga chimvano
Mukamadzalila ndidzasisima
Dzalitonthozeni kholo langa
Azibale anga, azinzanga
Written by: Eli Njuchi

Loading...