album cover
Ondi
album cover
Ondi è stato pubblicato il 16 maggio 2025 da Royal Image come parte dell'album Cifu
AlbumCifu
16 maggio 2025
EtichettaRoyal Image
BPM89
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia

Testi

Sxvage
Amakondwa onse akandiona, ondilandira ine
Chimwemwe ndi ziweto zomwe, ondilandira ine
Ndili ndi ana ondichingamira ndikafika Ndikanakonda akandione (Ndikanakonda akandione)
Kuli abale omwe andisowa komwe ndilunjikaku
Ndinakakonda akandione (Ndikanakonda akandione)
Imani nditsike, tsike, tsike, tikuthamangiranji?
Tikuthamangiranji?
Kuli bwino ndiyende, yende, yende, tikuthamangiranjiye
Tikuthamangiranjiye
A dalayvala Imani kaye eh heh, ndati ndifunse nawo
Mu galimoto muno, mu bus muno wachedwayo timudziwe nawo?
Tikuthawanji? Speed mpaka two hands mseu wake uti?
Ma overtake osaona kuti kuli bwanji, mseu wake uti?
Ndeno kupewa kuposa kuchiza
Sumutamika mukatigwetsa
Kuli bwino tikafike mochedwa osati ma bandagewo titamangidwa
Kuli abale omwe andisowa komwe ndilunjikaku
Ndikanakonda akandione, wa moyo akandione
Imani nditsike, tsike, tsike nanga tikuthamangiranjiye?
Tikuthamangiranjiye?
Kuli bwino ndiyende, yende, yende, tikuthamangiranjiye?
Tikuthamangiranjiye?
Imani nditsike, tsike, tsike nanga tikuthamangiranjiye?
Tikuthamangiranjiye?
Kuli bwino ndiyende, yende, yende, tikuthamangiranjiye?
Tikuthamangiranjiye?
Yeah
Tikuthamangiranji? Tikuthamangiranji?
Written by: Chifuniro Magalasi
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...