album cover
Eya
album cover
Eya è stato pubblicato il 16 maggio 2025 da Royal Image come parte dell'album Cifu
AlbumCifu
16 maggio 2025
EtichettaRoyal Image
BPM100
Melodicità
Acousticità
Valence
Ballabilità
Energia

Testi

I'ts Trex
(Trex, Trex, Trex...)
Eya ndibwela
Eya ndibwela
Eya, eya, eya
Musakaike kunyumba ndibwela
(ooh ndibwela, ey) ndibwela
Nane mami ndakusowani
Ndatsala pang'ono, pang'ono chabe
Musakaike kunyumba ndibwela
Ooh-ooh!
Eya ndibwela
Eya ndibwela (oh-ah)
Eya, eya, eya
Musakaike kunyumba ndibwela
Mumandidzutsa mam'mawa
Kwacha bwanji ku Joni ko?
Mumadziwa ndikanama
Nde mumachivumbulutsa chi pemphero
Mumayimba phone daily
Mumandipemphelera daily
Mwati mwezi wa nyuwere
Mwana wanga iwe ubwere
Ndikubwe- era, ndikubwera mama
Sindidumphitsa holiday
Ndikubwera mama
Ndatsala pang'ono, pang'ono chabe
Musakaike kunyumba ndibwela
Ooh-ooh!
Eya ndibwela
Eya ndibwela (oh-ah)
Eya, eya, eya
Musakaike kunyumba ndibwela
Ooh-ooh!
Eya (ooh-ooh!)
Ndibwela (ooh-ooh!)
Eya (ooh-ooh!)
Ndibwela (oh-ah)
Ndatsala pang'ono, pang'ono chabe
Musakaike kunyumba ndibwela
Mkamabwera mgulako ka chitenje
Mami mudzatcheneko thukuta langa
M'dzandiphikire limanda
Written by: Chifuniro Magalasi
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...