Lyrics

Unandipeza ndili lova Ndilibe kalikonse Mmatumba mwanga mobooka Nyumba yopanda khonde Ndekuti dzuwa likaomba Mkati khuma kumaonda Iweyo utandiona Sindimvetsa chomwe unakonda Utabwela unandilimbikitsa Unati ndisabwelele m'mbuyo Chomwe chinali chako naneso ndi changa Kuti ndisamasowe tulo You must be a saint or something How could you give it all And ask for nothing in return Ndikusowa chonena ine Malangizo ako Andifikitsa pena ine Poti ndiine wako Bwela umunyadile mamuna amene ndili Kamba ka iwe Bwela umunyadile mamuna amene ndili Kamba ka iwe For I was never enough I had room for you in my life Ndizizwa ndichisankho chako ooh Chokhala nane ngakhale mnyumba mwanga Mpando munalibe Pomwe sizinkandiyendela Unagwada ndikupemphela Pamene mwayi unatetela Unandiuza ndimukumbuke namalenga Ndikamabwela ku ulenje Mmalo mwa nyama ndi denje Nkumandilandilabe ndi chimwemwe Ine pakamwa kakasi You know pena ndikati ndidye frus Most of my days I am under the weather But I believe God gave you to me To help me keep it together You must be a saint or something How could you give it all And ask for nothing in return Ndikusowa chonena ine Malangizo ako Andifikisa pena ine Poti ndine wako Bwela umunyandile mamuna amene ndili Kamba ka iwee Chikondi ndachimvesesa Bwela umunyandile mamuna amene ndili Kamba ka iwee Nkhawa zonse unathesa Bwela umunyandile mamuna amene ndili Kamba ka iwee Chikondi ndachimvesesa Bwela umunyandile mamuna amene ndili Kamba ka iwee I'm a better man Sindikanakwanitsa ndekha I needed you to get me to where I am right now Ndikusowa chonena ine Malangizo ako Andifikisa pena ine Poti ndine wako Bwela umunyandile mamuna amene ndili Kamba ka iwe Bwela umunyandile mamuna amene ndili Kamba ka iwe
Writer(s): Kelvin Zalimba Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out