Lyrics

Yeah... Alright Ndidzala mawu anu pakamwa pangapa Nditama inu pakusuntha kwa lilaka Manjenje ayi paliponsepo ndiponda Ndiwope ndani poti ndinu ngaka yanga Baba you supply Zonse zomwe ndimasowa Kuyesa kufotokoza Ayi mpaka dzuwa litalowa Everybody knows Baba you supply Zonse zomwe ndimasowa Kuyesa kufotokoza Ayi mpaka dzuwa litalowa Chisomo chanu chandizungulira Oyiwalidwa mwamukumbukira Zomwe mumanena ndikhulupilira Ndikhulupilira malonjezo anu mukwaniritsa Ife tingoti Amen Aye Amen Aye Malonjezo anu Amen Aye Amen Aye Mukwaniritsa Amen Aye Amen Aye All your promises are Amen Aye Amen Aye Aye Aye Aye Aye All your promises are Aye Aye Aye Aye All your promises are Ndikhulupira chilichonse mumakamba Pazinkhanira mudzayala gome langa Oh when you say it is well You never retract Mumalizitsa ntchito yomwe mumayamba Baba you supply Zonse zomwe ndimasowa Kuyesa kufotokoza Mpaka dzuwa litalowa Everybody knows Baba you supply Zonse zomwe ndimasowa Kuyesa kufotokoza Ayi mpaka dzuwa litalowa Chisomo chanu chandizungulira Oyiwalidwa mwamukumbukira inu Baba Zomwe mumanena ndikhulupilira Ndikhulupilira malonjezo anu mukwaniritsa Ife tingoti Amen Aye Amen Aye Malonjezo anu Amen Aye Amen Aye Mukwaniritsa Amen Aye Amen Aye All your promises are Amen Aye Amen Aye Aye Aye Aye Aye All your promises are Aye Aye Aye Aye All your promises are Amen Aye Amen Aye All your promises are Aye Aye Aye Aye
Writer(s): Kelvin Zalimba Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out