Credits

COMPOSITION & LYRICS
Praise Umali
Praise Umali
Songwriter

Lyrics

I keep coming back for more
Like my heart’s addicted to seeing you go
And I’ve been trying to walk away
But my heart boomerang boomerang
There’s every reason to go but my heart choose to stay
Choose to stay
My heart choose to stay
Choose to stay
My heart choose to stay
Umangokhalabe iwe
Kodi bwanji umangokhalabe iwe
Kodi unandidyetsa konda ine, konda ine
Unandidyetsa konda ine, konda ine
Nanga bwanji ndimakonda iwe konda iwe konda iwe, konda iwe
Unandidyetsa konda ine konda ine, konda ine
Bwanji ndimakonda iwe konda iwe konda iwe, konda iwe
Unandidyetsa konda ine konda ine, konda ine
Yeah
Anthu akuti you bad for me now, baby
Iwe ndi ndimu ine ndi mkaka, Ching’ombe
Anthu akuti you not for me no, yeah
Iwe ndi moto ine ndi nthaka, uchoke
Choose to stay
My heart choose to stay
Choose to stay
My heart choose to stay
Choose to stay
My heart choose to stay
Choose to stay
My heart choose to stay
Still I choose to stay
My heart choose to stay
Umangokhalabe iwe
Kodi bwanji umangokhalabe iwe
Kodi unandidyetsa konda ine, konda ine
Unandidyetsa konda ine, konda ine
Nanga bwanji ndimakonda iwe konda iwe konda iwe, konda iwe
Unandidyetsa konda ine konda ine, konda ine
Bwanji ndimakonda iwe konda iwe konda iwe, konda iwe
Unandidyetsa konda ine konda ine, konda ine
Choose to stay
My heart choose to stay
Choose to stay
My heart choose to stay
Choose to stay
My heart choose to stay
Choose to stay
My heart choose to stay
Still I choose to stay
My heart choose to stay
Umangokhalabe iwe
Kodi bwanji umangokhalabe iwe iwe iwe
Kodi unandidyetsa konda ine, konda ine
Unandidyetsa konda ine, konda ine
Nanga bwanji ndimakonda iwe konda iwe konda iwe, konda iwe
Unandidyetsa konda ine konda ine, konda ine
Nanga bwanji ndimakonda iwe konda iwe konda iwe, konda iwe
Unandidyetsa konda ine konda ine, konda ine
Written by: Praise Umali
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...