album cover
Bodza
1,011
Afro-Beat
Bodza was released on July 31, 2022 by 1684208 Records DK as a part of the album Red Flag
album cover
Release DateJuly 31, 2022
Label1684208 Records DK
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM95

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Eli Njuchi
Eli Njuchi
Songwriter

Lyrics

Yah ndatseka chitseko
Eya yukumveka
Njuchi
Ish koma yah
Savage on the beat
Ish koma yah
Munalowa bodza mu nyumbamo
Kuyambira makolo ndi anawo
Ndinampeza mpaka mgwanya wapa gate
Amalandira ma tip kwa azi ancle
Munalowa chibodza munyumbamo
Kuyambira makolo ndi anawo
Makolo amangoti mwana ali kugeri
Osadziwa anadya fees kalekale
Abambo amadzivuta pa Malawi
Akati akakatenge kapambali
Anafika pomasinthitsa galimoto
Anthu asawazindikire m'makuka mu
Amayi akuvutika pa Malawi
Akati akakholetse kapambali
Mtima umakhala uli panja ku gate
Akangomva ka horn asuzumile
Koma palowa bodza, bodza
Bodza pa Malawi
Palowa bodza, bodza
Bodza pa Malawi
Bodza likutizunza pa Malawi
Bodza likutiphetsa pa Malawi
Palowa bodza, bodza
Bodza pa Malawi
Mwalowa kunama mu mpinngo mu
Chopeleka chanu mu mpingo mu
Chikumalowa purse ya chemwali
Chitukuko chapa church chagwela ena (ena)
Lero tipumeko za ndale
Za ndale takamba dzana kalekale
Kuja ndi kuchimake kwa zonsezi
Chitukuko chapa mudzi chagwera ena
Amachikunga chi bodza make Juniour
Ndili ku night service ali bwandilo
Amachikunga chi bodza bambo awo
Akati ataye ring kuma hotel
Bea wakumbali mu telephone
Anasevedwa Waterboard or ESCOM
Bea wakumbali mu telephone
Anasevedwa Champions league, wina zankhonde
Ndati palowa bodza, bodza
Bodza pa Malawi
Palowa bodza, bodza
Bodza pa Malawi
Bodza likutizunza pa Malawi
Bodza likutiphetsa pa Malawi
Palowa bodza, bodza
Bodza pa Malawi
Anthu akuphaka chi life pa social media
Handsome pa hd picture pokha
Tilipo ambiri okapsa
Akazi akufela bodza pa Malawi
Ndati palowa bodza, bodza
Bodza pa Malawi
Palowa bodza, bodza
Bodza pa Malawi
Bodza likutizunza pa Malawi
Bodza likutiphetsa pa Malawi
Palowa bodza, bodza
Bodza pa Malawi
Kwalowa bodza ku Malawi
Sispense iwe
Written by: Eli Njuchi
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...