album cover
Benz
album cover
Benz was released on September 25, 2026 by Royal Image as a part of the album Maga
AlbumMaga
ReleasedSeptember 25, 2026
LabelRoyal Image
BPM103
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Speed (speed, speed, speed)
(Umakonda ama benzi, wo)
Chanose dem
Pano ndine wamu benzi, yo
Umakonda ama benzi, wo
Baby, yeah
Unakangondiuza
Kuti umafuna wa ndalama
Unakangondiuza
Kuli umafuna wama benzi
Unakangondiuza
Kuti watopa ndi kabaza, baby
Mdakati udikire pang'ono, chabe
Unakangondiuza
Kuti baby limbikako
Unakangondiuza
Kuti baby gula yako
Unalikana dzulo langa
Udamutsika paso wanga
Wona lero langa ndili m'benzi, yeah-yeah-yeah
Today
Don't love my today, baby
Today
Don't you love my today, baby
Unakangondiuza
Unakangondiuza
Unakangondiuza
Umakonda ama benzi (ama benzi, ama benzi)
Umakonda ama benzi (ama benzi, ama benzi)
Umakonda ama benzi iwe (ama benzi iwe)
Umakonda ama benzi iwe (ama benzi iwe)
Umakonda ama (ama)
Padzulo, unawamvela azinzako, baby
Padzulo, anati undisiye ndine m'phawi, baby
Nde lero, wafuna wu passanger princess, baby (haha)
Benzi uyimvela fungo, chabe
Unakangondiuza
Kuti baby limbikako
Unakangondiuza
Kuti baby gula yako
Unalikana dzulo langa
Unayitsika paso yanga, baby (paso yanga)
Lero langa ndili m'benzi, yeah-yeah-yeah
Today
Don't love my today, baby
Today
Don't you love my today, baby
Unakangondiuza
Unakangondiuza
Unakangondiuza
Umakonda ama benzi iwe
Umakonda ama benzi iwe (ama benzi iwe)
Pano ndine wamu benzi, yo (wamu benz, yo)
Umakonda ama benzi, yo
Yeah, yeah (yeah, yeah)
(Umakonda ama benzi iwe)
(Pano ndine wamu benzi, yo)
(Umakonda ama benzi iwe)
(Ooh-ooh, Ooh-ooh)
Written by: Chifuniro Magalasi

Loading...