album cover
Wakuba (Interlude)
album cover
Wakuba (Interlude) was released on April 3, 2023 by Crispy Malawi as a part of the album Rnb
AlbumRnb
ReleasedApril 3, 2023
LabelCrispy Malawi
LanguageEnglish
BPM
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Aku recorder ndi Yashie
Iwe aku recorder ndi Yashie
Iwe aku recoder ndi Yashie
Wakuba
Amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (Eh)
Mkazi wakumpanda koma looks ndipanja wakunja (Yea)
Olo kumuloleza amatenga mwakuba
Koma ali safe ali m'manja mwakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Kumu caller Dirty ati iyeyo ali kwa Duda
Kuyithoka boys yanga ati samasuta
Koma amazanditenga kuvaya kwa plug koma kusonkha yamafuta
Ndimadya ndine koma kungoti ghetto simakhuta
Malo si ake koma ndadabwa wamasuka
Attention yanga sinduyiwona ndani wasunga? (Yeah)
Atha kubela mpweya iwe ndikubanika
Ofunika Kumu searcher uyu akamapita (Mh)
(Yeah, yeah) Nde akamavina mpamene umaziwa kuti ass yangodzadza ndi ma fats
Amangokwiya ati ndimachulutsa ma facts
Pa TikTok ndimafila fukwa ali ndi chi nyash
Olo mbina ndamudabwa mene wanyamulira
Waba uku koma uku nkomwe wajudukira
Timuphika fukwa watibela chopakulira
Waba moto fanzi ikuwona ngati wazimitsira
Wakuba
Amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (Eh)
Mkazi wakumpanda koma looks ndipanja wakunja (Yea)
Olo kumuloleza amatenga mwakuba
Koma ali safe ali m'manja mwakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Written by: Chifundo Chingaipe, Prince Ntaya
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...