album cover
Kusangalala
19,763
Dance
Kusangalala was released on December 8, 2023 by Money Making Music exclusively distributed under Serato Media Group (Pty) Ltd as a part of the album For The Streets
album cover
Release DateDecember 8, 2023
LabelMoney Making Music exclusively distributed under Serato Media Group (Pty) Ltd
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM111

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Robert Ching’amba
Songwriter

Lyrics

Eyoh tiyeni
Tiyeni tiyeni tiyeni eish
Una-na-na
Una-na-na mmh
Una-na-na
Una-na-na mmh
Pomwe ena akulira ena akuseka mmh
Pomwe ena akulira ena akusekelera
Koma masiku ako osekelera sangakhale onse dziwa
Ndati masiku ako ovutika sangakhale onse dziwa
Zokhumudwitsa ndi zambiri
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri
Koma ine ndasankha kusangalala
Olo ndidzilira! ndilira mpaka liti?
Ndidzidandaula! ndidandaula mpaka liti?
Olo ndidzilira! Ndilira mpaka liti? (ndilira mpaka liti)
Olo ndidzidandaula! mmh mpaka liti (ndidandaula mpaka liti)
Poti mavuto samatha, mavuto samatha
Mavuto samatha, mavuto samatha
Mavuto samatha, mavuto samatha
Mavuto samatha, mavuto samatha
Zokhumudwitsa ndi zambiri
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri
Koma ine ndasankha kusangalala
Zokhumudwitsa ndi zambiri
Koma ine ndasankha kusangalala
Kusangalala, kusangalala
Kusangalala, kusangalala
Kusangalala, kusangalala
Written by: Robert Ching’amba
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...