Credits
COMPOSITION & LYRICS
Ian Derrick Ngalande
Songwriter
Hope Cizzle Ngalande
Songwriter
Lyrics
Ngini Ili Sharp Taphusha
Ndi boys yanga ija tikalinka
Timaichemesa ife tikafika
Timasiya nkhani ife tikadusa
Ngini Ili Sharp Taphusha
Ndi boys yanga ija tikalinka
Timaichemesa ife tikafika
Timaichemesa ife tikafika
Tikupanga Udolo
Boys yamenya call
Tatipeze chapa Chanco
Tagwetsa Kale Mabotolo Folo
Tikupanga Udolo
Boys yamenya call
Tatipeze chapa Chanco
Tagwetsa Kale Mabotolo Folo
Tikuphusha Ngini Khala Ngati Cardio
Tikusuntha Trynna Get Money
Ngati Sadio
On another level
Nyimbo zathu munvela pa radio
Cerebrity Status, Ma hater Outside
Ali Panja
Koma Tikangofika
Pachema Pachema
Koma Tikangofika
Patentha Patentha
Koma Tikangofika
Pachema Pachema
Koma Tikangofika
Patentha Patentha
Written by: Hope Cizzle Ngalande, Ian Derrick Ngalande