album cover
Maloto
93
Dance
Maloto was released on June 22, 2026 by Hit Factory Records, Exclusively Distributed Under Trappybeats. & Hope Cizzle. (Pty) Ltd as a part of the album Maloto - Single
album cover
Release DateJune 22, 2026
LabelHit Factory Records, Exclusively Distributed Under Trappybeats. & Hope Cizzle. (Pty) Ltd
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM114

Credits

PERFORMING ARTISTS
Trappybeats.
Trappybeats.
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Hope Cizzle.
Hope Cizzle.
Songwriter
Ian Derrick Ngalande
Ian Derrick Ngalande
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Trappybeats.
Trappybeats.
Executive Producer

Lyrics

Panali Nthawi Kale
Tikuseka Osaganiza Zambiri
Kucheza Kukamba Nthano
Kumunda Kuthyola Nkhwani
Ndi Anzanga Kuumba Dongo
Nkhawa Tilibe, Tilibe
Pena Kugona Ndi Njala (Ndaonapo)
Anzanga Kundisala (Ndaonapo)
Abale Kundikana
(Ndaonapo, Ndaonapo)
Pena Kugona Ndi Njala
Anzanga Kundisala
Abale Kundikana
(Ndaonapo, Ndaonapo)
Sizili Monga Kale
Moyo Wasintha, Koma ine sindikusintha
Stay True To Myself
Ndikukumbukila Kale
Nthawi Imene Ndinka Chaser Maloto!
Sizili Monga Kale
Moyo Wasintha, Koma ine sindikusintha
Ndikukumbukila Kale
Nthawi Imene Ndinka Chaser Maloto!
I was busy chasing dreams back then
Even on the weekends aaah aaah
Ambiri simungamvetse pano mungoti ndine superstar superstar aaah
Let's take it back to the basics
Nditadziwana ndi achina Sispence
Anandiuza mfana uli ndi talent
Ungofunika kuzipanga market
Pano Jah Jah anadalitsa dalitsa! Pano nginiii!
Sizili Monga Kale
Moyo Wasintha, Koma ine sindikusintha
Stay True To Myself
Ndikukumbukila Kale
Nthawi Imene Ndinka Chaser Maloto!
Sizili Monga Kale
Moyo Wasintha, Koma ine sindikusintha
Ndikukumbukila Kale
Nthawi Imene Ndinka Chaser Maloto!
Written by: Hope Ngalande, Ian Ngalande
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...