Music Video
Music Video
Credits
PERFORMING ARTISTS
Crispy Malawi
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Chifundo Chingaipe
Composer
PRODUCTION & ENGINEERING
x3l
Producer
Ayo Landie
Mixing Engineer
Lyrics
ndili ndi Anzanga tikungosuta chamba
koma ndi anzanga sitimangosuta Chamba
ntima suvala sanza,nde ukavaya shopping
uzitha kusankha
ukafuna mkazi wachi figure
uzitha ku flipa numbers
uzi pusher Dancehall osamangosuta Chamba
apa Homie Akundipasa move ya ndalama
koma ali busy akupota chamba
zomwe amakamba sangokamba amazipanga
koma kwawo amangot amangosuta Chamba
Anzanga Eni eni Anandipasa kale ma flowers
amandipilira ku woker nane late hours\spenaldo ndi hero ali ndima super powers
ena anasiya mowa ndi mkamwa nawo powers
ndili ndi Anzanga tikungosuta chamba
koma ndi anzanga sitimangosuta Chamba
ntima suvala sanza,nde ukavaya shopping
uzitha kusankha
ukafuna mkazi wachi figure
uzitha ku flipa numbers
uzi pusher Dancehall osamangosuta Chamba
Written by: Chifundo Chingaipe