album cover
Kachasu
album cover
Kachasu was released on August 20, 2025 by Brainlock T-Kas,Under Exclusive License to a’ba.lé Sound System as a part of the album From Chinsapo With Love - EP
August 20, 2025
LabelBrainlock T-Kas,Under Exclusive License to a’ba.lé Sound System
BPM
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

265
Benjamin
Ayo Landie
Ndimakhala ghetto koma sindisipper kachasu
Ndili ndi ma guys ama sipper ama amabandaso
Ena Ndi amu ghetto ena amashala mumpandaso
Amadziwa life ndima G's samadadanso
Olo amwe nip, gin olo kachasu
Spender zonse night Kunja Kwacha ku chaser kwachaso
Boys yanga sizamva lero tiyakaso
Lighter ilipo mu bag mwadzadza zazaso
Home boy wangoyima pa que Tingopanga za gaso
Certified trapper koma tikupusher ma dancehall
Tonse timayimba koma ife timayimba mwakaso
Ndi kuwoneka fresh ndalinker Ndi Themba kwa Chinsapo
Nduziwa ma babe a bho a ghetto oti ama slayer
Akalowa city center mtengo unakwera
Amatrapper Ndi big boys yambiri yobleya
Naneso ndi wa ghetto zambiri sindinena (Shh)
Tonse tiku hasser koma ena akuba (Wakuba)
Akutsutsa lunso langa samtha kumva
Anali Ndi mkazi wa bho chinamuluma chakuda
Ali Café 92 akungosipper chakumwa
Si rapper wabho nde ghetto inamukanaso
Akukakamiza uptown koma chizungu samathaso
Akulenga ka-no mind koma samabandaso
Iwe Spe tawawuze tachoka kwa Chinsapo
Ndimakhala ghetto koma sindisipper kachasu
Ndili ndi ma guys ama sipper ama amabandaso
Ena Ndi amu ghetto ena amashala mumpandaso
Amadziwa life ndima G's samadadanso
Olo amwe nip, gin olo kachasu
Spender zonse night Kunja Kwacha ku chaser kwachaso
Boys yanga sizamva lero tiyakaso
Lighter ilipo mu bag mwadzadza zazaso
Ayo
Benjamin
We ain't got no time
Hahah
Written by: Crispy Malawi, Themba Kasambara
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...