Credits
PERFORMING ARTISTS
Daniel Khoviwa
Keyboards
Titus Mizaya
Drums
Judah Mkandawire
Bass
COMPOSITION & LYRICS
Kelvin Zalimba
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Humphreys Mkandawire
Producer
Timothy Dalitso Mizaya
Producer
Lyrics
VERSE 1
Nditamanda dzina lanu tsiku ndi tsiku
Tate wanga
Pokuti ndinu munalenga zamoyo mapiri
Ndi nyanja
Ati ndinu architecture
Zaumwini wanu zovuta kumvetsa
Ati ndinu protector
Mfumu yokhayo yopanda successor
Mumatiimilila pamene mdyelekezi akufuna kutizenga mulandu
Lawyer wama lawyer ndinu tate
Munalenga messi painuyo sangamake
God of love
Sikuti ndiozikonda koma alibe nzake
Nkona ndigwada
Kumutamanda
Hook
Ulemu upite kumwamba
Kumwamba x3
Ndinali ndani popanda
Popanda x3
Chisomo chake
Jehovah ndinu nangula x2
Moyowu ndinu munagula x2
VERSE 2
Mulungu wanga sasewela ndi coach
Amandikonza ndikalakwitsa
Kuwala mumdima chimozi mozi
Pamaso pake palibe chobisika
Ndi mphunzitsi waophunzitsa
Mwiniwake wazozizwitsa
Bata panyanja
Zonse mwapanga
Ndiombela mmanja
Imela baba!!
Sing'anga wanga ndimaombeza kwaaaaa
Akwanilitsa zomwe wa lonjeza kwaa
Lonjeza kwa ine
God of love yeah
Sikuti ndiozikonda koma alibe mzake
Nkona ndinagwada
Nkumutamanda
HOOK
Ulemu upite kumwamba
Kumwamba x3
Ndinali ndani popanda
Popanda x3
Chisomo chake
Jehovah ndinu nangula x2
Moyowu ndinu munagula x2
BRIDGE
Azibambo ng'oma zilile
Azimayi ombani mmanja
Tiyeni timulambile
Mulengi okhala mmwamba
Azibambo ng'oma zilileee eh
Tiyeni timulambile eehh
HOOK
Ulemu upite kumwamba
Kumwamba x3
Ndinali ndani popanda
Popanda x3
Chisomo chake
Jehovah ndinu nangula x2
Moyowu ndinu munagula x2
Ending
Written by: Kelvin Zalimba