album cover
Mwadala
album cover
Mwadala was released on June 13, 2025 by Les Disques Bongo Joe as a part of the album Ma Gitala
June 13, 2025
LabelLes Disques Bongo Joe
BPM
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Music Video

Music Video

Lyrics

Pamane Timakhala pa dziko lapansi
Panali munthu wina dzina lake a Tiyese
A Tiyese anali osauka
Abale awo akawasala
A Tiyese Mwadala
Kuti chifukwa Mwadala
Muli ndi mwai
Mudzipephera, Mudzithokoza
A Tiyese anali opephera
A Tiyese anali olombika
Pogwira ntchito ndi manja awo
Potero atate anawapatsa
Potero ambuye anawadalitsa
Chuma chawo, lero siawo
Atate anadalitsa
Mwadala, mwadala, mwadala
When we were on this world
There was this man called Tiyese
Tiyese was a poor person
His relatives scolded him
Tiyese your blessed
Because your blessed
You got lucky
Continue praying and be thankful
Tiyese was a prayerful person
Tiyese was a hardworker
Working so hard with his hands
In that way, the father gave him
That way he was blessed.
With his wealth, look at him now
Father blessed him
Your blessed, blessed, blessed
Written by: Yobu Maligwa, Yosefe Kalekeni
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...