album cover
Dzuwa
album cover
Dzuwa was released on May 16, 2025 by Royal Image as a part of the album Cifu
AlbumCifu
May 16, 2025
LabelRoyal Image
BPM130
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

(O-O-OBK Beats)
Bwanji tingovomeleza
Kuti inde mdandinamiza
Bwanji tingovomeleza
Kuti inde mdandipusitsa
Mama musanagone
Mdati ndisadandaule
Mdati tidzaonanaso
Ndingodikira, ndingodikira
Bwanji tingovomeleza
Kuti inde mdandinamiza
Bwanji tingovomeleza
Kuti inde mudawina ndinuyo
Dad musadagone
Mudandiuza ndisalire
Mdati tidzakumanaso
Ndingodikira, ndingodikira
Ndadikira
Mpaka dzuwa ndilo
Ndilo likulowa
Mdakadikira
Ndikudikirabe
Ndadikira (aah)
Mpakana maluwa (wa)
Ndi awa akufota (ine)
Mdakadikira
Ndikudikirabe
Mdati ndikatole nkhomo
Mudzandiphunzitse kuyenda bawo
Nditabwela ndapeza mwagona
Ndikudikirabe
Ndikudikirabe
Mudati ndikule pang'ono
Mudzandiphunzitse kutchova njinga
Mpaka ndakula inu mukadagona
Ndikudikirabe
Ndikudikirabe
Mudati ndilimbike sukulu (mpaka dzuwa ndilo)
Mdzandiyimbire ng'oma pa gara (ndilo likulowa)
Gara ndi inoyo (kulibe, kulibe)
Dad musanagone
Mudandiuza ndisalire
Mdati tidzakumananaso
Ndingodikira, ndingodikira
Ndadikira
Mpaka dzuwa ndilo (dikirabe)
Ndilo likulowa
Mdakadikirabe
Ndikudikirabe
Ndadikira (kudikirabe)
Mpakana maluwa (ndungodikirabe)
Ndi awa akufota (ine)
Mdakadikirabe
Ndikudikirabe
Ndadikira (kudikirabe)
Mpaka dzuwa ndilo
Ndilo likulowa
Mdakadikirabe
Ndikudikirabe
Ndadikira (aah)
Mpakana maluwa (aah)
Ndi awa akufota (ine)
Mdakadikirabe
Ndikudikirabe
Written by: Chifuniro Magalasi
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...