album cover
Kuyimba
Dance
Kuyimba was released on January 29, 2026 by Mwankisi as a part of the album SINCE XVIII - EP
album cover
Release DateJanuary 29, 2026
LabelMwankisi
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM100

Music Video

Music Video

Credits

PERFORMING ARTISTS
Mwankisi
Mwankisi
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Ntulitutule Matandala
Ntulitutule Matandala
Composer

Lyrics

Nyimbo za Ife ase ndi zo hita
Sungafananize ndi makape
Zomwe ama spita
Ife tinapita
Sungatiuze chochita ase
Kuchoka 2018 pomwe tinayamba Ife kuyimba
Nde sungatipeze tikusekelera
Sitimasekelera ngakhale beat
Uzafunse marie kapena jane
Uzandipeza nditango dekha
Nyimbo Ife timayimba
Ena amango dzinva
Nyimbo Ife timayimba
Ena amango dzinva
Nyimbo Ife timayimba
Zimawapweteka mimba
Nyimbo Ife timayimba
Ndinayambila mimba
Sungatiuze chochita
Mene ife tinayambila ase
Timangopitilira Peter Mutharika
Pano ndingopitilira sindiyima ase
Virus za ine ukudziwa iwe
Makape iwe ase tawasiye iwe
Ndinali ndi ka mkazi
Kananditelera nakauza kuti ase
Ndiwe woyelekedwa ukufuna kuti... Zindidelera
Ati Celebrity ngati mkazi akakuteleke
Nangoti ase zikuyendere
Nangopanga zoti zindiyendere koma
Nyimbo Ife timayimba
Ena amango dzinva
Nyimbo Ife timayimba
Zimawapweteka mimba
Nyimbo Ife timayimba
Ena amango dzinva
Nyimbo Ife timayimba
Zimawapweteka mimba
Nyimbo Ife timayimba
Zimawapweteka mimba
Nyimbo Ife timayimba
Ena amango dzinva
Nyimbo Ife timayimba
Ena amango dzinva
Nyimbo Ife timayimba
Ena amango dzinva
Written by: Ntulitutule Matandala
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...