album cover
YEAR0
Hip-Hop/Rap
YEAR0 was released on January 29, 2026 by Mwankisi as a part of the album YEAR0 - Single
album cover
Release DateJanuary 29, 2026
LabelMwankisi
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM139

Credits

PERFORMING ARTISTS
Mwankisi
Mwankisi
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Ntulitutule Matandala
Ntulitutule Matandala
Composer

Lyrics

Black Fire I wanna use it as a target
Ndakoka YEAR0
Akukana chotsa mwado
Ndiwa mwano ndimuchotsa mano
Ndimadana ndi kano akukuta mano
Ngati watsika pano ndimukwera pano
Watsala Ntipa anachota nsalu
Wotetha ngati ngabu
Ineso ndi wa Hot ine si rajah wa medium
Medium
Ma Scammer ma social media mu media mu
Ndakoka YEAR0
Akukana chotsa mwado
Ndiwa mwano ndimuchotsa mano
Ndimadana ndi kano akukuta mano
Ngati watsika pano ndimukwera pano
Ndakoka YEAR0
Akukana chotsa mwado
Ndiwa mwano ndimuchotsa mano
Ndimadana ndi kano akukuta mano
Ngati watsika pano ndimukwera pano
Ngati watsika pano ndimukwera pano
Ndimadana ndi kano
Uziwakale pachi Malawi opanda tsankho
Situkamba za awo iwe tukamba za pano
Iwe
Ndakoka YEAR0
Akukana chotsa mwado
Ndiwa mwano ndimuchotsa mano
Ndimadana ndi kano akukuta mano
Ngati watsika pano ndimukwera pano
Ndakoka YEAR0
Akukana chotsa mwado
Ndiwa mwano ndimuchotsa mano
Ndimadana ndi kano akukuta mano
Ngati watsika pano ndimukwera pano
Black Fire I wanna use it as a target
Written by: Ntulitutule Matandala
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...