album cover
Lighter
15
Hip-Hop/Rap
Lighter was released on May 23, 2023 by Wazizur as a part of the album Tailora
album cover
AlbumTailora
Release DateMay 23, 2023
LabelWazizur
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM90

Music Video

Music Video

Credits

PERFORMING ARTISTS
Suffix
Suffix
Rap
COMPOSITION & LYRICS
Suffix
Suffix
Songwriter
Barnie Michael
Barnie Michael
Lyrics
PRODUCTION & ENGINEERING
Barnie Michael
Barnie Michael
Producer

Lyrics

Heyayayaya
Heyayaya
Heyayaya
Heyayayaya
Yah, wazizur
It's 10 in the morning
Build up ya african cup pa Super sport
Ma neba panjapa akuti odi
Pa den pali dstv ndife ma doni
Bozi nafe timadoda
Ku team yathu ndife madoda
Olo ah coach akama coacher
Amanditcha ateacher kufewa ngati okocha
Big za mpira samazifila
Masten ndi big zampirazi imazifila
Pan'gono
Ati bola geli nzilimbikila
Vuto langa ku balansa nthawi kumandiKhila
Amwene kuno gaba wa chinyatu
Ndi sha sha gaba kuno nafenso tikuwina
Ah ah kodi iwe kugeli kuja unapita
Ndi nzako uja mmamgokhalira mpira ndi kuimba tazibwera kuno
My little lighter
Iwo sangaione
Koma za adela za adela amazifila
My little lighter
Iwo sangaione
Koma za adela za adela amazifila
Maganizo anga ndoti
Zimabebaaa ukakhala ndi po gwi
Zikazakuvuta uzaitchola plan b
NdiPaMpanje pano dolo osamaphweketsa geli
Enawa amamva kukoma ukamakalanyatu
Getting wasted ati ulowe live cha mma past 2
Ukang'alure iwo ali busy kusakasaka ma school
Ukazitolera azikubifaa ati azagenda kwanu mxii
Zimakoma akakhala wa nzako
Woimba wa za ma comedy akakhala si wako
Wako umamupusha azipanga sukulu
Wanzako nkumamupopa akamaimba m'ma sukulumu of course
Of course there's no formula
Utha kuiphula opanda degree olo diploma yah komano
Ma chancewo nde ndi eh eh
Zibwana nje ukakhala ndi Mwai opanga geli
My little lighter
Iwo sangaione
Koma za adela za adela amazifila
My little lighter
Iwo sangaione
Koma za adela za adela amazifila
Written by: Aubrey Suffix Ghambi, Barnie Michael
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...