album cover
Tinazituluka
album cover
Tinazituluka was released on June 25, 2026 by 13056262 Records DK as a part of the album Tinazituluka - Single
June 25, 2026
Label13056262 Records DK
LanguageEnglish
BPM96
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Mkhani za chikondi zipangani
Koma ngati zili za party tiyitaneni
Mkhani za chikondi tiye nazoni
Koma ngati zili za ku church tiwuzeni
Chifungwa izi izi, tinazituluka pano
Mza satanic, tinazituluka mmmm!
Ife izi-izi, tinazituluka pano
Ndipo zimamwa magazi, tinazituluka
N'nayesako kukonda mamuna zomwe
Na kumana nazo
Sindisiyanisa mwa mamuna dikambuku Mwamuna akamati, mayi ndakukondani
Ndimawona chinsato, chikulilima kwa mbili
Mwaukali kundipenya kufuna kumeza ine
Ndevu zake zimandiwonekela ngati mavu wooo! woluma mogwesa chifufu ngakhale njovu
Mkhani za chikondi zipangani
Koma ngati zili za party tiyitaneni
Mkhani za chikondi tiye nazoni
Koma ngati zili za ku church tiwuzeni
Chifungwa izi izi, tinazituluka pano
Mza satanic, tinazituluka mmmm!
Ife izi-izi, tinazituluka pano
Ndipo zimamwa magazi, tinazituluka
N'nayesapo kukonda mkazi zomwe nakumana nazo sindisiyanitsa mwamkazi ndi lithumbu
When a woman mmmm! me green lights, I feel a sense of fear in my mind
Coz ndimaona ngati volcano waphulika pankhani zachikondi ndimamva mtima kuthamanga komanso kuchepa kwa magazi chizungulile mkati mmmm!
Mkhani za chikondi zipangani
Koma ngati zili za party tiyitaneni
Mkhani za chikondi tiye nazoni
Koma ngati zili za ku church tiwuzeni
Chifungwa izi izi, tinazituluka pano
Mza satanic, tinazituluka mmmm!
Ife izi-izi, tinazituluka pano
Ndipo zimamwa magazi, tinazituluka
Mmmm!
Tinazituluka pano
Mza satanic, tinazituluka mmmm!
Tinazituluka pano
Ndipo zimamwa magazi, tinazituluka
Mmmm!
Written by: Man Chi Chiwambo
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...