album cover
Hindi
Afro-Pop
Hindi was released on June 25, 2026 by 13056262 Records DK as a part of the album Hindi - Single
album cover
Release DateJune 25, 2026
Label13056262 Records DK
LanguageHindi
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM92

Credits

PERFORMING ARTISTS
Man Chi Chiwambo
Man Chi Chiwambo
Background Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Man Chi Chiwambo
Man Chi Chiwambo
Composer
PRODUCTION & ENGINEERING
Man Chi Chiwambo
Man Chi Chiwambo
Engineer
Witty Fam
Witty Fam
Executive Producer

Lyrics

lAaaa! aaaaaaaa!
man chi chiwambo
Ana anachokela balaka
anakhala ana ovuta kulelaaaa
Chi, wa, m'bandidelela imwe mdaizimbo ng'ona imwe
Abuluzi amu water cane zikhale ng'ona
Njuchi zakulunzu pa ken zikhale ng'oma
Inu a nep ma guitar ayi ken zikhale ng'oma
Titokote pa tiktok ken sikale koma
Woba ma lyric asandisathe sina size yawo ine
Ndimayenda ndekha sindiyenda ndi munthu bawo ine
Asandimange sindiyenda ndi anthu akubawo ine
Akandipange add zaku mtundu kwawo ine
Kuli msonkhano Wazimayi Kuzomba Ku chingale
Waitanitsa msonkhano ndi norman chisali
Chi anti-tiwo ndibwere nacho noman chisale
Kuwuthawa ulimi eti no man chizale
Man Chi
मलावी का अकेला म्यूज़िशियन
— man chi!
जो हिंदी बोलता है
— man chi!
किसी से तुलना नहीं कर सकते
— man chi!
भारत के लोग भी मेरा नाम जानते हैं
— man chi!"
Ndi mtengo wa zipatso nkona chilichonse chakwera
Ka sugar ndi nasunga et kajesi kabwera
Mnapita ku india mnakafika mumumbai Ndampeza vitumbiko mukutani mumumbai
Ma punch amenewawa ndi mnzake wa b j ayi si jize
ndimfana wa ziwindi Atha kuyambana ndi pamza waziwindi ngati jelly bro
मलावी, तुमने मेरी संगीत को कम आंका, लेकिन मेरी स्टाइल अनोखी है। मैं मलावी के किसी की नकल नहीं करता — यह मेरी अपनी स्टाइल है, मलावियन इंडिया से।
—man chi!
_man chi!
—man chi!
_man chi!
man chi!
मलावी का अकेला म्यूज़िशियन
— man chi!
जो हिंदी बोलता है
— man chi!
किसी से तुलना नहीं कर सकते
— man chi!
भारत के लोग भी मेरा नाम जानते हैं
— man chi!
यह भारत में नहीं है। आपने किसी ऐसे व्यक्ति को देखा है जो उसके जैसा दिखता है, लेकिन वह वही व्यक्ति नहीं है। आप गलत हैं, मुझ पर विश्वास कीजिए।
Written by: Man Chi Chiwambo
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...