album cover
Kuno
album cover
Kuno was released on July 25, 2025 by Manifest as a part of the album Twenty Somethxngs
July 25, 2025
LabelManifest
LanguageEnglish
BPM192
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Call inabwela
Ati
“hello ukundimva? Ine amami”
Ine ndati hello Masteni
Ati
“ndikale unaimba phone,
Ndati ndikupatse moni.
Uli bwanji mwananga?
Kodi kufumbi kuli bwanji mwananga?”
Ine ndati ndili welo kuno
Amami ndili welo kuno
Inde pena zikuvuta kuno
Pena moyo ukushupa kuno
Ati
“kukula ndi choncho mwananga
Dziwa moyo ndi choncho mwananga
Kuti pena zimayenda
Pena zimavuta
Koma udzipemphera
Udzipemphera
Kumapemphera
Udzipemphera”
Written by: Praise Umali

Loading...