Lyrics

Man wo nda bhobho Si andewu ngati achina thompo Amatchilaso mwa bhobho Komano mkaziyoo Mkaziyo ndi wangwilo Amafunika superhero Komano man wo akumabwera ndi yawo yawo Komano amtenga aah Inuyo mupenga aa Komano antenga aah Inuyo mupeeee (nga) Komano amtenga Winayo watenga Inuyo mupenga Winayo wa nteee ee (nga) Mkaziyo ndi wa bhobho Komano man wooo Alibe khalidwe Mkazi amangomenya Daily kugona ndi nkhawa Kenako mudanda akathawa Koma pena pake kumavomeleza Onani bondo mwa nong'oneza Yeeah Lalalalalalala amutenga ena Lalalalalalalala amutenga ena Man wo nda bhobho Si andewu ngati achina thompo Amatchilaso mwa bhobho Komano mkaziyoo Mkaziyo ndi wangwilo Amafunika superhero Komano man wo akumabwera ndi yawo yawo Komano amtenga aah Inuyo mupenga aa Komano antenga aah Inuyo mupeeee (nga) Iii inu ma man Iii inu tamvani Iii inu pali nkhani Kwavuta Kumutsiku Akuchita kungananana Malaya kukwenyanana Koma amavanana (nana) Iyeeeeeh Kulipo kuona ngati amakukonda Komano utazisandusa wekha mlonda Care for your partner suzapitaso kwa wina aah Man wo nda bhobho Si andewu ngati achina thompo Amatchilaso mwa bhobho Komano mkaziyoo Mkaziyo ndi wangwilo Amafunika superhero Komano man wo akumabwera ndi yawo yawo Komano amtenga aah Inuyo mupenga aa Komano antenga aah Inuyo mupeeee (nga) Care for your partner Care for your partner Care for your partner aaaah Ayye Maone Awosh
Writer(s): Zonke Mhone Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out