Music Video

Music Video

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Robert Ching’amba
Songwriter

Lyrics

Eyo VJ, eish!
Tiyeni, tiyeni
Tiyeni, tiyeni, tiyeni eish!
Pita, ukanene ndathela pano
Anthu onsewa adziwe, ndathela pano
Ndati pita, ukanene ndathela pano
Anthu onsewa adziwe, ndathela pano
Ndiye undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Ndati undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Akabwela kudzafunsa, usamangike iwe
Awuze adziwe, uli ndi ine
Akabwela kudzafunsa, usamangike iwe
Awuze adziwe, uli ndi ine
Poti ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndiye Pita ukanene, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati pita ukanene, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano eish
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Ndati undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Undikonde, mopanda mantha pozindikila ulipo wekha
Akabwela kudzafunsa, usamangike iwe
Awuze adziwe, uli ndi ine
Akabwela kudzafunsa, usamangike iwe
Awuze adziwe, uli ndi ine
Ndiye pita ukanene, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati pita ukanene, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano eish
Ndati ndathe, ndathe, ndathela pano
Ine ndathe, ndathe, ndathela pano
Written by: Robert Ching’amba
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...