Lyrics

Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu Ayiwala zonse, tinakambilana zija Ayiwala zonse, tinalambilana zina eish Ayiwala zonse, ndinawapangila zija Ayiwala zonse, ndinawapangila zija Apeza wanyowani, avuta mma status Apeza wanyowani ndiye avuta mma status Apeza wanyowani, avuta mma status Apeza wanyowani ndiye avuta mma status Ngati ndakutopetsa Vuto ndi chani, osangondiuza Koma kungochoka osanena, unangondiyuza Ngati ndakutopetsa Vuto ndi chani, osangondiuza Koma kungochoka osanena, unangondiyuza eish! Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu Ayiwala zonse, tinakambilana zija Ayiwala zonse, tinalambilana zina eish Ayiwala zonse, ndinawapangila zija Ayiwala zonse, ndinawapangila zija Apeza wanyowani, avuta mma status Apeza wanyowani ndiye avuta mma status Apeza wanyowani, avuta mma status Apeza wanyowani ndiye avuta mma status Ngati ndakutopetsa vuto ndi chani, osangondiuza Koma kungochoka osanena, unangondiyuza Ngati ndakutopetsa vuto ndi chani, osangondiuza Koma kungochoka osanena, unangondiyuza eish! Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu Alamu anu, alamu anu, anangochoka alamu anu Alamu anu, alamu anu anangochoka alamu anu Ayiwala zonse, tinakambilana zija Ayiwala zonse, tinalambilana zina eish Ayiwala zonse, ndinawapangila zija Ayiwala zonse, ndinawapangila zija Apeza wanyowani, avuta mma status Apeza wanyowani ndiye avuta mma status Apeza wanyowani, avuta mma status Apeza wanyowani ndiye avuta mma status
Writer(s): Robert Ching'amba Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out