album cover
Illuminat
682
New Age
Illuminat was released on March 16, 2019 by 1684208 Records DK as a part of the album Illuminat - Single
album cover
Release DateMarch 16, 2019
Label1684208 Records DK
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM196

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Eli Njuchi
Eli Njuchi
Songwriter

Lyrics

Yeah yeah yeah yeah ooh
Aaah ooh oh ooh!
Uh yeah yeah
Uh yeah yeah
Silver, Njuchi
Kunali chimdima
Ndidadabwa kadzanja kakundikodola
Nditawonetsetsa anali mkazi wokongola
Timawu tamtatamya mkudzati tandilondola
I still feel 'dem
Ndili munjira adayamba kundiuza nkhani
Eli uli ndi luso labho chamkatikati
Tikudziwa wakumana ndi zokhoma
But we don't know ngati unaganizirako za
Illuminat, Eli Njuchi mpaka alowe
Illuminat, kuti ma babe amufile
Nyimbo zake zimveke
Akhale mfana wo riser oti amagona pa zeke alowe
Illuminat illumina-illumina illuminat
Me don't know now
Me fighting fi a long time but nothing upon my side, illuminat
She started saying things like she was reading my mind
Ukango joiner wapeza ulemelero
Upeza zonse zomwe umafunitsitsa zija
Ugwira chimkazi chomwe umafuna chija
Zomwe tikufuna kwa iweyo ndi zochepa
Ungozimitsa a Chizmo ndi a Veda
Komaso tifuna a Chifuniro aja
Nditavomela kunatseguka chikhomo
Kunali chiphwando
Zomwe ndimkaona zinali zachilendo
Kudabwana Dada Chai-Khun ali pampando
Ndekuti nzika zinalandila kale udindo (Njuchi)
Mr Kauden anabweletsa mbale
Ndinanyamula mpeni oti ineyo ndibayile
Ndinalira nditawona abale anga
Akumenya pemphero lawo la madzulo
Illuminat, Eli Njuchi mpaka alowe
Illuminat, kuti ma babe amufile
Nyimbo zake zimveke
Akhale mfana wo riser oti amagona pa zeke alowe
Illuminat illumina-illumina illuminat
Me don't know now
Me fighting fi a long time but nothing upon my side, illuminat
Kunali chimdima
Ndidadabwa kadzanja kakundikodola
Nditaonetsetsa anali mkazi wokongola
Timawu tamtatamya mkudzati tandilondola
I still feel 'dem
Ndili munjira adayamba kundiuza nkhani
Eli uli ndi luso labho chamkatikati
Tikudziwa wakumana ndi zokhoma
But we don't know ngati unaganizirako za
Illuminat, Eli Njuchi mpaka alowe
Illuminat, kuti ma babe amufile
Nyimbo zake zimveke
Akhale mfana wo riser oti amagona pa zeke alowe
Illuminat illumina-illumina illuminat (yeah yeah yeah)
Me don't know now (Eli)
Me fighting fi a long time but nothing upon my side, illuminat
Eyo Zuka
Me don't know
Written by: Eli Njuchi
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...